On Air Feature

Chinyanja News

Date: Sep 22, 2021

News,current affairs,sports in Chinyanja

MITU YA NKANI MU NDIME YA ZOCHITIKA MU AFRICA 

For more Chinyanja News programmes, click here:

 

MAGULU LA AZIMAYI KU DZIKO LA ZAMBIA AKHAZIKITSA MABUNGWE OSUNGA NDALAMA  

Zambian women benefiting from village banking

 

CHINYANJA:  Magulu azimayi mu nzinda wa Lusaka mdziko la Zambia abwera pamodzi mogwirizana ndi kukhazikitsa mabungwe awo osunga ndalama zimene pakapita kanthawi maguluwa amazagawana

ENGLISH:  Most women are benefiting from village banking in Zambia

 

CMC YALEMBELA KALATA MLEMBI WA OFESI YA MTSOGOLERI WA MALAWI PA NKHANI YA MISEWU

Human rights organisation in Malawi urges presidency to monitor roads authority operation

CHINYANJA:  Bungwe lomenyela ufulu wa anthu ku Malawi la Center for Mindset Change (CMC) lalembela chikalata mlembi wa ofesi ya mtsogoleri ndi nduna zaboma chokhuzana ndi kagwiridwe ka ntchito ka adindo oyendetsa bungwe loyang’anila misewu la Roads Authority, muchikalatachi lapatsa mlembiyu matsiku khumi ndi anayi kuti achitepo kanthu

ENGLISH: Human rights organisation in Malawi Center for Mindset Change has urged the presidency to monitor how the Department of Roads Authority operates. 

 

ANTHU AKUPITILIZA KUGWIRITSA NTCHITO MA ANTIBIOTICS MOSASAMALA KU ZAMBIA

Illegal abuse of antibiotics on rise in Zambia

CHINYANJA : Nduna ya za umoyo ku Zambia Sylivia Masebo yati anthu akupitiliza mchitidwe ogwiritsa ntchito mankhwala a ma Anti-biotics mwachisawawa ndipo izi zimabweretsa chiophyezo chachikulu mmatupi a anthu

ENGLISH:  Health minister in Zambia Sylivia Masebo says illegal abuse of antibiotics is on the rise in the country.

 

GRACE MUGABE WAGONJA PA MLANDU OKUMBA MANDA A ROBERT MUGABE  

Grace Mugabe lose court case

CHINYANJA :  Mkazi wa mtsogoleri wa kale wa dziko la Zimbabwe Grace Mugabe wagonja pa mlandu okumba manda a mtsogoleriyu yemwe anaikidwa ku muzi wa Zimba. Khothi la ku chigawo cha Chinhoyi lagamula kuti manda a Mugabe akumbidwe ndipo akaikidwe ku manda a ngwazi kapena kuti Heroes Acre

ENGLISH: Grace Mugabe has lost a court case in which she wanted the body of  her husband Robert Mugabe to  remain in Zvimba in Zimbabwe.

 

MALAWI PRISON SERVICE IKULINGALILA KUBAYISA AKAIDI 10 000 KATEMELA WA COVID-1

Malawi’s prisons to vaccinate 10 000 prisoners

CHINYANJA :  Nthambi yoyang’anira ndende mdziko la Malawi ya Malawi Prison Services yati ikulingalila kubayisa akaidi okwana 10 000 katemela wa matenda a Covid-19 mu ndende zosiyana siyana za mdzikolo

ENGLISH:  Malawi’s prison services plans to inoculate 10 000 prisoners with Covid 19 vaccine.

 

MUUNI WA ZA MIYAMBO  

Ancient marriage values still practiced in Mozambique.

Mozambique continue to practice ancient marriage

CHINYANJA :  Anthu mdziko la Mozambique amatsatilabe miyambo yosiyana siyana yamakolo  mmabanja mwawo 

ENGLISH:    Ancient marriage values are still practiced in Mozambique.

Comments

comments powered by Disqus

Web Content Viewer (JSR 286)

Actions
Loading...

ADVERTISEMENT

Web Content Viewer (JSR 286)

Actions
Loading...
Complementary Content
CLOSE

Your Name:*

Your Email:*

Your Message:*

Enter Captcha:*